Salimo 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, lengani mtima wolungama mkati mwanga,+Ndipo ikani maganizo* atsopano ndi okhazikika mwa ine.+ Ezekieli 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala m’matupi awo+ n’kuwapatsa mtima wamnofu,+ Ezekieli 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tayani zolakwa zanu zonse zimene munachita+ ndipo muyesetse kukhala ndi mtima watsopano+ ndiponso mzimu watsopano.+ Kodi muferenji+ inu a nyumba ya Isiraeli?’ Aroma 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musamatengere+ nzeru za nthawi* ino, koma sandulikani mwa kusintha maganizo anu,+ kuti muzindikire+ chimene chili chifuniro+ cha Mulungu, chabwino, chovomerezeka ndi changwiro.
10 Inu Mulungu, lengani mtima wolungama mkati mwanga,+Ndipo ikani maganizo* atsopano ndi okhazikika mwa ine.+
19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala m’matupi awo+ n’kuwapatsa mtima wamnofu,+
31 Tayani zolakwa zanu zonse zimene munachita+ ndipo muyesetse kukhala ndi mtima watsopano+ ndiponso mzimu watsopano.+ Kodi muferenji+ inu a nyumba ya Isiraeli?’
2 Musamatengere+ nzeru za nthawi* ino, koma sandulikani mwa kusintha maganizo anu,+ kuti muzindikire+ chimene chili chifuniro+ cha Mulungu, chabwino, chovomerezeka ndi changwiro.