Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiponso malamulo amene amapereka imfa,+ amenenso analembedwa pamiyala,+ anabwera ndi ulemerero waukulu kwambiri+ moti ana a Isiraeli sanathe kuyang’anitsitsa nkhope ya Mose chifukwa inali kuwala ndi ulemerero,+ ulemerero umene unatha patapita nthawi.

  • 2 Akorinto 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Tonsefe+ tili ndi nkhope zosaphimba ndipo tili ngati magalasi oonera amene amaonetsa ulemerero wa Yehova.+ Pamene tikuonetsa ulemerero umenewu, timasintha+ n’kukhala ngati chifaniziro chake+ ndipo timaonetsa ulemerero wowonjezerekawonjezereka+ mofanana ndendende ndi mmene Yehova, amene ndi Mzimu, watisinthira.+

  • 2 Akorinto 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti Mulungu ndiye anati: “Kuwala kuunike kuchokera mu mdima,”+ ndipo kudzera mwa nkhope ya Khristu,+ waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudzana ndi kudziwa+ Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena