Aroma 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 momwemonso ifeyo, ngakhale kuti ndife ambiri, tili thupi limodzi+ mwa Khristu, ndipo aliyense payekha ndi chiwalo cha mnzake.+ Aefeso 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma polankhula zoona,+ tiyeni tikule m’zinthu zonse, kudzera m’chikondi,+ pansi pa iye amene ndi mutu,+ Khristu.
5 momwemonso ifeyo, ngakhale kuti ndife ambiri, tili thupi limodzi+ mwa Khristu, ndipo aliyense payekha ndi chiwalo cha mnzake.+
15 Koma polankhula zoona,+ tiyeni tikule m’zinthu zonse, kudzera m’chikondi,+ pansi pa iye amene ndi mutu,+ Khristu.