Aroma 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero ndikukudandaulirani mwa chifundo chachikulu cha Mulungu abale, kuti mupereke matupi anu+ ngati nsembe+ yamoyo,+ yoyera+ ndi yovomerezeka kwa Mulungu,+ ndiyo utumiki wopatulika+ mwa kugwiritsa ntchito luntha la kuganiza.+ 1 Akorinto 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano inu ndinu thupi la Khristu, ndipo aliyense wa inu ndi chiwalo cha thupilo.+ Aefeso 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kuti awongolere oyerawo,+ achite ntchito yotumikira, amange thupi la Khristu,+
12 Chotero ndikukudandaulirani mwa chifundo chachikulu cha Mulungu abale, kuti mupereke matupi anu+ ngati nsembe+ yamoyo,+ yoyera+ ndi yovomerezeka kwa Mulungu,+ ndiyo utumiki wopatulika+ mwa kugwiritsa ntchito luntha la kuganiza.+