15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Nyamuka uzipita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa chochita kusankhidwa+ chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina,+ komanso kwa mafumu+ ndi ana a Isiraeli.
8 (pajatu iye amene anapatsa Petulo mphamvu yokhala mtumwi kwa anthu odulidwa ndi amene anapatsanso ine mphamvu+ kuti ndikalalikire kwa anthu a mitundu ina)