Machitidwe 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo Agiripa anauza Fesito kuti: “Inenso ndikufuna ndimve ndekha munthu ameneyu+ akulankhula.” Iye anati: “Mawa mudzamumvetsera.” Machitidwe 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Agiripa+ anauza Paulo kuti: “Waloledwa kulankhula mbali yako.” Pamenepo Paulo anatambasula dzanja lake+ ndi kuyamba kulankhula modziteteza kuti:+ Machitidwe 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndi kunena kuti, ‘Usaope Paulo. Uyenera kukaima pamaso pa Kaisara,+ ndipo taona! Chifukwa cha iwe, Mulungu mokoma mtima adzapulumutsa onse amene uli nawo pa ulendowu.’
22 Pamenepo Agiripa anauza Fesito kuti: “Inenso ndikufuna ndimve ndekha munthu ameneyu+ akulankhula.” Iye anati: “Mawa mudzamumvetsera.”
26 Ndiyeno Agiripa+ anauza Paulo kuti: “Waloledwa kulankhula mbali yako.” Pamenepo Paulo anatambasula dzanja lake+ ndi kuyamba kulankhula modziteteza kuti:+
24 ndi kunena kuti, ‘Usaope Paulo. Uyenera kukaima pamaso pa Kaisara,+ ndipo taona! Chifukwa cha iwe, Mulungu mokoma mtima adzapulumutsa onse amene uli nawo pa ulendowu.’