1 Akorinto 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kukoma mtima kwakukulu+ ndi mtendere+ zochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Yesu Khristu Ambuye wathu+ zikhale ndi inu. Agalatiya 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo onse otsatira lamulo limeneli la mmene tiyenera kukhalira, amene ndi Isiraeli wa Mulungu, akhale ndi mtendere ndiponso chifundo.+ 2 Yohane 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tidzalandira kukoma mtima kwakukulu,+ chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate+ wathu ndi kwa Yesu Khristu Mwana wa Atate, limodzi ndi choonadi ndiponso chikondi.+
3 Kukoma mtima kwakukulu+ ndi mtendere+ zochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Yesu Khristu Ambuye wathu+ zikhale ndi inu.
16 Ndipo onse otsatira lamulo limeneli la mmene tiyenera kukhalira, amene ndi Isiraeli wa Mulungu, akhale ndi mtendere ndiponso chifundo.+
3 Tidzalandira kukoma mtima kwakukulu,+ chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate+ wathu ndi kwa Yesu Khristu Mwana wa Atate, limodzi ndi choonadi ndiponso chikondi.+