1 Timoteyo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndikulembera iwe Timoteyo,+ mwana wanga weniweni+ m’chikhulupiriro: Kukoma mtima kwakukulu, chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi Khristu Yesu Ambuye wathu, zikhale nawe.+ 2 Timoteyo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndikulembera iwe Timoteyo mwana wanga wokondedwa:+ Kukoma mtima kwakukulu, chifundo, ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi kwa Khristu Yesu Ambuye wathu+ zikhale nawe.
2 ndikulembera iwe Timoteyo,+ mwana wanga weniweni+ m’chikhulupiriro: Kukoma mtima kwakukulu, chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi Khristu Yesu Ambuye wathu, zikhale nawe.+
2 ndikulembera iwe Timoteyo mwana wanga wokondedwa:+ Kukoma mtima kwakukulu, chifundo, ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi kwa Khristu Yesu Ambuye wathu+ zikhale nawe.