Aroma 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 momwemonso ifeyo, ngakhale kuti ndife ambiri, tili thupi limodzi+ mwa Khristu, ndipo aliyense payekha ndi chiwalo cha mnzake.+ 1 Akorinto 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi simukudziwa kuti matupi anu ndiwo ziwalo+ za Khristu?+ Ndiye kodi ine nditenge ziwalo za Khristu n’kuzisandutsa ziwalo za hule?+ Zosatheka zimenezo! Aefeso 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 umene ndi thupi lake.+ Mpingowo ndi wodzaza+ ndi iye, amene amadzaza zinthu zonse mokwanira.+
5 momwemonso ifeyo, ngakhale kuti ndife ambiri, tili thupi limodzi+ mwa Khristu, ndipo aliyense payekha ndi chiwalo cha mnzake.+
15 Kodi simukudziwa kuti matupi anu ndiwo ziwalo+ za Khristu?+ Ndiye kodi ine nditenge ziwalo za Khristu n’kuzisandutsa ziwalo za hule?+ Zosatheka zimenezo!