1 Akorinto 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi simukudziwa kuti matupi anu ndi ziwalo za Khristu?+ Ndiye kodi ine nditenge ziwalo za Khristu nʼkuzichititsa kukhala ziwalo za hule? Zosatheka zimenezo!
15 Kodi simukudziwa kuti matupi anu ndi ziwalo za Khristu?+ Ndiye kodi ine nditenge ziwalo za Khristu nʼkuzichititsa kukhala ziwalo za hule? Zosatheka zimenezo!