Yohane 6:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Palibe munthu angabwere kwa ine akapanda kukokedwa ndi Atate amene anandituma ine,+ ndipo ine ndidzamuukitsa tsiku lomaliza.+ 2 Akorinto 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu mwa kufuna kwa Mulungu, ndikulembera mpingo wa Mulungu wa ku Korinto, pamodzi ndi oyera onse+ amene ali mu Akaya+ monse, ndili limodzi ndi Timoteyo+ m’bale wathu, kuti:
44 Palibe munthu angabwere kwa ine akapanda kukokedwa ndi Atate amene anandituma ine,+ ndipo ine ndidzamuukitsa tsiku lomaliza.+
1 Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu mwa kufuna kwa Mulungu, ndikulembera mpingo wa Mulungu wa ku Korinto, pamodzi ndi oyera onse+ amene ali mu Akaya+ monse, ndili limodzi ndi Timoteyo+ m’bale wathu, kuti: