1 Timoteyo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndikulembera iwe Timoteyo,+ mwana wanga weniweni+ m’chikhulupiriro: Kukoma mtima kwakukulu, chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi Khristu Yesu Ambuye wathu, zikhale nawe.+ 2 Yohane 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tidzalandira kukoma mtima kwakukulu,+ chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate+ wathu ndi kwa Yesu Khristu Mwana wa Atate, limodzi ndi choonadi ndiponso chikondi.+
2 ndikulembera iwe Timoteyo,+ mwana wanga weniweni+ m’chikhulupiriro: Kukoma mtima kwakukulu, chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi Khristu Yesu Ambuye wathu, zikhale nawe.+
3 Tidzalandira kukoma mtima kwakukulu,+ chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate+ wathu ndi kwa Yesu Khristu Mwana wa Atate, limodzi ndi choonadi ndiponso chikondi.+