Aroma 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndikulembera inu nonse amene muli ku Roma monga okondedwa a Mulungu, oitanidwa+ kukhala oyera:+ Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere+ wochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye wathu Yesu Khristu+ zikhale ndi inu.
7 Ndikulembera inu nonse amene muli ku Roma monga okondedwa a Mulungu, oitanidwa+ kukhala oyera:+ Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere+ wochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye wathu Yesu Khristu+ zikhale ndi inu.