Danieli 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero amuna amphamvuwa anati: “Danieliyu sitingamupezere chifukwa chilichonse. Ngati tikufuna kumupezera chifukwa, chikhale chokhudzana ndi lamulo la Mulungu wake.”+ Maliko 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Yesu anati: “Perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma zinthu za Mulungu muzizipereka kwa Mulungu.”+ Ndipo iwo anadabwa naye kwambiri.+ 1 Petulo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa cha Ambuye, gonjerani+ dongosolo lililonse lopangidwa ndi anthu:+ kaya mfumu+ chifukwa ili ndi udindo waukulu,
5 Chotero amuna amphamvuwa anati: “Danieliyu sitingamupezere chifukwa chilichonse. Ngati tikufuna kumupezera chifukwa, chikhale chokhudzana ndi lamulo la Mulungu wake.”+
17 Pamenepo Yesu anati: “Perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma zinthu za Mulungu muzizipereka kwa Mulungu.”+ Ndipo iwo anadabwa naye kwambiri.+
13 Chifukwa cha Ambuye, gonjerani+ dongosolo lililonse lopangidwa ndi anthu:+ kaya mfumu+ chifukwa ili ndi udindo waukulu,