Machitidwe 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Paulo anati: “Yohane anabatiza anthu ubatizo umene unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Anali kuuza anthu kuti akhulupirire amene anali kubwera m’mbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.” Aroma 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kapena simudziwa kuti tonsefe amene tinabatizidwa ndipo tsopano tili mu mgwirizano ndi Khristu Yesu+ tinabatizidwanso mu imfa yake?+
4 Pamenepo Paulo anati: “Yohane anabatiza anthu ubatizo umene unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Anali kuuza anthu kuti akhulupirire amene anali kubwera m’mbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.”
3 Kapena simudziwa kuti tonsefe amene tinabatizidwa ndipo tsopano tili mu mgwirizano ndi Khristu Yesu+ tinabatizidwanso mu imfa yake?+