-
Agalatiya 2:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Popeza tikudziwa kuti munthu amayesedwa wolungama+ mwa kukhulupirira+ Khristu Yesu, osati chifukwa cha ntchito za chilamulo, ife takhulupirira Khristu Yesu. Tachita zimenezi kuti tiyesedwe olungama chifukwa cha chikhulupiriro chathu mwa Khristu,+ osati mwa ntchito zotsatira chilamulo. Tatero chifukwa palibe munthu adzayesedwa wolungama chifukwa cha ntchito zotsatira chilamulo.+
-