Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 15:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Pakuti chokhoza kuwonongekachi chidzavala kusawonongeka,+ ndipo chokhoza kufachi+ chidzavala kusafa.

  • Aheberi 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti bambo athu otiberekawo, kwa masiku ochepa anali kutilanga malinga ndi zimene anaziona kuti n’zoyenera,+ koma Mulungu amatilanga kuti tipindule ndiponso kuti tikhale oyera ngati iyeyo.+

  • 1 Petulo 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Anatibereka kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka,+ chosadetsedwa ndiponso chosasuluka. Cholowa chimenechi anasungira inuyo kumwamba,+

  • 1 Yohane 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Okondedwa, tsopano ndife ana a Mulungu,+ koma padakali pano sizinaonekerebe kuti tidzakhala otani.+ Tikudziwa kuti akadzaonekera,+ tidzakhala ngati iyeyo,+ chifukwa tidzamuona mmene alili.+

  • Chivumbulutso 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena