1 Petulo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho, ndikulangiza akulu amene ali pakati panu mowadandaulira, pakuti inenso ndine mkulu+ ngati iwowo. Ndinenso mboni+ ya masautso a Khristu, ndiponso ndidzalandira nawo ulemerero umene udzaonekere.+ Kwa iwo ndikuti: 3 Yohane 1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine monga mkulu,+ ndikulembera wokondedwa Gayo, amene ndimamukonda kwambiri.+
5 Choncho, ndikulangiza akulu amene ali pakati panu mowadandaulira, pakuti inenso ndine mkulu+ ngati iwowo. Ndinenso mboni+ ya masautso a Khristu, ndiponso ndidzalandira nawo ulemerero umene udzaonekere.+ Kwa iwo ndikuti: