1 Petulo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho, ndikulangiza akulu amene ali pakati panu mowadandaulira, pakuti inenso ndine mkulu+ ngati iwowo. Ndinenso mboni+ ya masautso a Khristu, ndiponso ndidzalandira nawo ulemerero umene udzaonekere.+ Kwa iwo ndikuti: 2 Yohane 1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine monga mkulu,+ ndikulembera mayi wosankhidwa+ ndi Mulungu ndiponso ana ake amene ndimawakondadi.+ Ndipo si ine ndekha amene ndimawakonda. Onse amene adziwa choonadi amawakondanso.+
5 Choncho, ndikulangiza akulu amene ali pakati panu mowadandaulira, pakuti inenso ndine mkulu+ ngati iwowo. Ndinenso mboni+ ya masautso a Khristu, ndiponso ndidzalandira nawo ulemerero umene udzaonekere.+ Kwa iwo ndikuti:
1 Ine monga mkulu,+ ndikulembera mayi wosankhidwa+ ndi Mulungu ndiponso ana ake amene ndimawakondadi.+ Ndipo si ine ndekha amene ndimawakonda. Onse amene adziwa choonadi amawakondanso.+