Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Amene sali kumbali yanga akutsutsana ndi ine, ndipo amene sasonkhanitsa anthu pamodzi ndi ine amawabalalitsa.+

  • 1 Yohane 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kodi wabodza angakhalenso ndani, kuposa amene amatsutsa kuti Yesu ndiye Khristu?+ Ameneyu ndiye wokana Khristu,+ amene amakana Atate ndi Mwana.+

  • 1 Yohane 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma mawu alionse ouziridwa amene amatsutsa zoti Yesu anabwera monga munthu, amenewo si ochokera kwa Mulungu,+ ndipo ndi ouziridwa ndi wokana Khristu amene munamva kuti akubwera,+ ndipo tsopano ali kale m’dziko.+

  • Yuda 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndatero chifukwa chakuti anthu ena alowa mozemba pakati pathu.+ Anthu amenewa Malemba anawasonyezeratu kalekale+ kuti adzaweruzidwa.+ Iwo ndiwo anthu osaopa Mulungu+ amene atenga kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu wathu kukhala chifukwa chochitira khalidwe lotayirira,+ ndipo akhala osakhulupirika+ kwa Ambuye wathu mmodzi yekha+ amene anatigula,+ Yesu Khristu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena