Ezekieli 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ananditengera kumeneko ndipo ndinaonako munthu wamwamuna. Munthuyo anali kuoneka wonyezimira ngati mkuwa.+ M’manja mwake munali chingwe cha fulakesi* ndi bango loyezera,+ ndipo anaima pachipata. Chivumbulutso 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndinapatsidwa bango lokhala ngati ndodo+ ndipo ndinauzidwa kuti: “Nyamuka, kayeze nyumba yopatulika ya pakachisi+ wa Mulungu, guwa lansembe, ndi amene akulambira mmenemo.
3 Kenako ananditengera kumeneko ndipo ndinaonako munthu wamwamuna. Munthuyo anali kuoneka wonyezimira ngati mkuwa.+ M’manja mwake munali chingwe cha fulakesi* ndi bango loyezera,+ ndipo anaima pachipata.
11 Ndiyeno ndinapatsidwa bango lokhala ngati ndodo+ ndipo ndinauzidwa kuti: “Nyamuka, kayeze nyumba yopatulika ya pakachisi+ wa Mulungu, guwa lansembe, ndi amene akulambira mmenemo.