Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 78:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Chifukwa cha iwo anachotsa mitundu ina pang’onopang’ono m’dzikoli,+

      Ndipo anayesa dzikoli ndi kuligawa kwa iwo kukhala cholowa chawo,+

      Moti anachititsa mafuko a Isiraeli kukhala m’nyumba zawozawo.+

  • Ezekieli 47:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno munthu uja anapita mbali ya kum’mawa atatenga chingwe choyezera m’manja mwake.+ Kenako anayeza mtsinjewo mikono 1,000 kuchokera pa Nyumba ija, ndipo anandiuza kuti ndiwoloke mtsinjewo. Madziwo anali olekeza m’mapazi.

  • Zekariya 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano ndinakweza maso ndipo ndinaona munthu ali ndi chingwe choyezera m’dzanja lake.+

  • Chivumbulutso 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno ndinapatsidwa bango lokhala ngati ndodo+ ndipo ndinauzidwa kuti: “Nyamuka, kayeze nyumba yopatulika ya pakachisi+ wa Mulungu, guwa lansembe, ndi amene akulambira mmenemo.

  • Chivumbulutso 21:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano amene anali kundilankhula uja ananyamula bango+ lagolide loyezera, kuti ayeze mzindawo, zipata zake, ndi mpanda wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena