Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anapachika makatani a nsalu, makatani opangidwa ndi thonje labwino kwambiri ndi makatani abuluu.+ Makataniwo anawamanga ndi zingwe zopangidwa ndi nsalu zabwino kwambiri ndi zingwe zaubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira.+ Zingwezi anazikulunga pamikombero yasiliva ndi pazipilala za miyala ya mabo. Anazikulunganso pamipando+ yagolide ndi siliva yokhala ngati mabedi. Mipandoyi inali pakhonde la miyala ya pofeli,* miyala yoyera ya mabo, ngale ndi miyala yakuda ya mabo.

  • Yobu 28:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mwala wamtengo wapatali wa korali+ ndi wa kulusitalo sizingayerekezedwe n’komwe ndi nzeruzo.

      Ndipo thumba lodzaza ndi nzeru ndi lamtengo wapatali kuposa thumba lodzaza ndi ngale.+

  • Mateyu 13:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Atapeza ngale imodzi yamtengo wapatali,+ anapita mwamsanga n’kukagulitsa zinthu zonse zimene anali nazo ndi kukagula ngaleyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena