Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Musawonjezepo kalikonse pa mawu amene ndikukulamulani, ndipo musachotsepo kalikonse pa mawu amenewa,+ kuti musunge malamulo a Yehova Mulungu wanu amene ndikukupatsani.

  • Deuteronomo 12:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Muzichita mosamala mawu onse amene ndikukuuzani.+ Musawonjezepo kapena kuchotsapo kalikonse.+

  • Miyambo 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Usawonjezere kanthu pa mawu ake+ kuti angakudzudzule ndiponso kuti ungakhale wabodza.+

  • Yohane 20:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kunena zoona, Yesu anachita zizindikiro zinanso zambiri pamaso pa ophunzirawo, zimene sizinalembedwe mumpukutu uno.+

  • 2 Akorinto 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chifukwa panopa wina akabwera kwa inu n’kulalikira za Yesu wosiyana ndi amene tinamulalikira,+ kapena wina akakubweretserani mzimu wosiyana ndi umene munalandira kale,+ kapena uthenga wabwino+ wosiyana ndi umene munaulandira, inu mumangomulolera munthu woteroyo.+

  • Agalatiya 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komabe, ngati ifeyo kapena mngelo wochokera kumwamba angalengeze nkhani ina kwa inu monga uthenga wabwino, koma nkhaniyo n’kukhala yosiyana ndi uthenga wabwino umene tinaulengeza kwa inu, ameneyo akhale wotembereredwa.+

  • 1 Yohane 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma mawu alionse ouziridwa amene amatsutsa zoti Yesu anabwera monga munthu, amenewo si ochokera kwa Mulungu,+ ndipo ndi ouziridwa ndi wokana Khristu amene munamva kuti akubwera,+ ndipo tsopano ali kale m’dziko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena