Chivumbulutso 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+
2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+