Chivumbulutso 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako, ndinaona mpukutu wolembedwa mkati ndi kunja komwe,+ uli m’dzanja lamanja la Iye wokhala pampando wachifumu.+ Unali womatidwa+ mwamphamvu ndi zidindo 7 zomatira.
5 Kenako, ndinaona mpukutu wolembedwa mkati ndi kunja komwe,+ uli m’dzanja lamanja la Iye wokhala pampando wachifumu.+ Unali womatidwa+ mwamphamvu ndi zidindo 7 zomatira.