Ezekieli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anautambasula pamaso panga, ndipo unalembedwa kuseri n’kuseri.+ Mumpukutumo munalembedwa nyimbo zoimba polira, mawu odandaula ndi mawu olira.+
10 Iye anautambasula pamaso panga, ndipo unalembedwa kuseri n’kuseri.+ Mumpukutumo munalembedwa nyimbo zoimba polira, mawu odandaula ndi mawu olira.+