Levitiko 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo m’mwezi wa 7, pa tsiku la 10 la mweziwo,+ muziliza lipenga la nyanga ya nkhosa lolira mokwera kwambiri.+ Muziliza lipenga la nyanga ya nkhosalo m’dziko lanu lonse pa tsiku lochita mwambo wophimba machimo.+ Numeri 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Upange malipenga+ awiri asiliva. Uchite kusula, ndipo uziwagwiritsa ntchito poitanitsa+ msonkhano ndi posamutsa msasa.
9 Ndipo m’mwezi wa 7, pa tsiku la 10 la mweziwo,+ muziliza lipenga la nyanga ya nkhosa lolira mokwera kwambiri.+ Muziliza lipenga la nyanga ya nkhosalo m’dziko lanu lonse pa tsiku lochita mwambo wophimba machimo.+
2 “Upange malipenga+ awiri asiliva. Uchite kusula, ndipo uziwagwiritsa ntchito poitanitsa+ msonkhano ndi posamutsa msasa.