Miyambo 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu wolungama akamanjenjemera pamaso pa munthu woipa, amakhala ngati kasupe woipitsidwa ndiponso chitsime chowonongedwa.+ Amosi 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mukuweruza mopanda chilungamo,+ choncho moyo wakhala wowawa ndi wosautsa kwa anthu, pakuti inuyo mwakana chilungamo.+ Amosi 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Kodi mahatchi angathamange pathanthwe, kapena kodi munthu angalime pathanthwe ndi ng’ombe? Anthu inu mwakana chilungamo,+ choncho mwachititsa moyo wa anthu kukhala wowawa.
26 Munthu wolungama akamanjenjemera pamaso pa munthu woipa, amakhala ngati kasupe woipitsidwa ndiponso chitsime chowonongedwa.+
7 Mukuweruza mopanda chilungamo,+ choncho moyo wakhala wowawa ndi wosautsa kwa anthu, pakuti inuyo mwakana chilungamo.+
12 “‘Kodi mahatchi angathamange pathanthwe, kapena kodi munthu angalime pathanthwe ndi ng’ombe? Anthu inu mwakana chilungamo,+ choncho mwachititsa moyo wa anthu kukhala wowawa.