Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 102:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kuti amve kuusa moyo kwa akaidi,+

      Ndi kumasula anthu opita kukaphedwa.+

  • Salimo 137:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 137 Tinakhala pansi+ m’mphepete mwa mitsinje ya ku Babulo,+

      Ndipo tinalira titakumbukira Ziyoni.+

  • Salimo 142:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Nditulutseni mundende ya mdima+

      Kuti nditamande dzina lanu.+

      Chititsani kuti anthu olungama asonkhane ndi kundizungulira,+

      Chifukwa mumandichitira zabwino.+

  • Yesaya 42:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 kuti ukatsegule maso a akhungu,+ ukatulutse mkaidi m’ndende ya mdima+ ndiponso kuti ukatulutse m’ndende anthu amene ali mu mdima.+

  • Yesaya 49:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 kuti ndiuze akaidi+ kuti, ‘Tulukani!’+ ndi amene ali mu mdima+ kuti, ‘Dziululeni!’+ Iwo adzadya msipu m’mphepete mwa msewu, ndipo m’mphepete mwa njira zonse zodutsidwadutsidwa mudzakhala malo awo odyeramo msipu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena