Yesaya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano taonani! Kukubwera magaleta ankhondo okokedwa ndi mahatchi awiriawiri, mutakwera amuna ankhondo.”+ Kenako iye anayamba kufuula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+ Yeremiya 51:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Babulo wagwa mwadzidzidzi moti wasweka.+ Mulireni mofuula anthu inu.+ M’patseni mafuta a basamu kuti muthetse ululu wake,+ mwina achira.” Chivumbulutso 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno mngelo wamphamvu ananyamula mwala wooneka ngati mphero yaikulu+ n’kuuponya m’nyanja,+ ndipo anati: “Mzinda waukulu wa Babulo udzaponyedwa pansi mofulumira ndi mwamphamvu chonchi, ndipo sudzapezekanso.+
9 Tsopano taonani! Kukubwera magaleta ankhondo okokedwa ndi mahatchi awiriawiri, mutakwera amuna ankhondo.”+ Kenako iye anayamba kufuula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+
8 Babulo wagwa mwadzidzidzi moti wasweka.+ Mulireni mofuula anthu inu.+ M’patseni mafuta a basamu kuti muthetse ululu wake,+ mwina achira.”
21 Ndiyeno mngelo wamphamvu ananyamula mwala wooneka ngati mphero yaikulu+ n’kuuponya m’nyanja,+ ndipo anati: “Mzinda waukulu wa Babulo udzaponyedwa pansi mofulumira ndi mwamphamvu chonchi, ndipo sudzapezekanso.+