Yeremiya 51:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Ndiyeno ukanene kuti, ‘Umu ndi mmene Babulo adzamirire osatulukanso chifukwa cha masoka amene ndikumugwetsera.+ Ndipo Ababulowo adzadzitopetsa okha.’”+ Mawu a Yeremiya athera pamenepa. Ezekieli 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Ndidzakugwetsera zoopsa modzidzimutsa+ ndipo sudzakhalaponso. Anthu adzakufunafuna+ koma sudzapezeka mpaka kalekale,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
64 Ndiyeno ukanene kuti, ‘Umu ndi mmene Babulo adzamirire osatulukanso chifukwa cha masoka amene ndikumugwetsera.+ Ndipo Ababulowo adzadzitopetsa okha.’”+ Mawu a Yeremiya athera pamenepa.
21 “‘Ndidzakugwetsera zoopsa modzidzimutsa+ ndipo sudzakhalaponso. Anthu adzakufunafuna+ koma sudzapezeka mpaka kalekale,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”