Chivumbulutso 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako mngelo wachiwiri analiza lipenga lake. Ndipo chinachake chokhala ngati phiri lalikulu+ limene likuyaka moto chinaponyedwa m’nyanja.+ Moti gawo limodzi mwa magawo atatu a nyanja, linasanduka magazi.+
8 Kenako mngelo wachiwiri analiza lipenga lake. Ndipo chinachake chokhala ngati phiri lalikulu+ limene likuyaka moto chinaponyedwa m’nyanja.+ Moti gawo limodzi mwa magawo atatu a nyanja, linasanduka magazi.+