Yeremiya 51:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tinafuna kuchiritsa Babulo, koma iye sanachiritsike. Tiyeni timusiye anthu inu+ ndipo aliyense wa ife apite kudziko lakwawo.+ Pakuti chiweruzo chake chafika kumwamba ndipo chakwera kufika m’mitambo.+ 1 Timoteyo 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Machimo a anthu ena amaonekera poyera,+ ndipo zimenezi zimachititsa kuti aweruzidwe. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pambuyo pake.+
9 “Tinafuna kuchiritsa Babulo, koma iye sanachiritsike. Tiyeni timusiye anthu inu+ ndipo aliyense wa ife apite kudziko lakwawo.+ Pakuti chiweruzo chake chafika kumwamba ndipo chakwera kufika m’mitambo.+
24 Machimo a anthu ena amaonekera poyera,+ ndipo zimenezi zimachititsa kuti aweruzidwe. Koma anthu ena, machimo awo amadzaonekera pambuyo pake.+