Masalimo
Iye wavala ulemerero.+
Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+
Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+
3 Inu Yehova, mitsinje ikufuula.
Ikufuula ndi mawu amphamvu.+
Mitsinje ikupitiriza kufuula ndi mawu amkokomo.+