Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 14
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

1 Akorinto 14:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:1
  • +Aro 12:6; 1At 5:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1993, tsa. 31

1 Akorinto 14:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:5
  • +1Ak 13:2

1 Akorinto 14:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 10:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2010, ptsa. 24-25

1 Akorinto 14:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:30
  • +Yow 2:28; Mac 2:17; 21:9
  • +1Ak 12:10

1 Akorinto 14:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 1:12; 2:2
  • +1Ak 12:8; 2Ak 11:6

1 Akorinto 14:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yob 21:12

1 Akorinto 14:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nu 10:9; Yob 39:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2015, tsa. 21

1 Akorinto 14:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:19
  • +1Ak 9:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2015, tsa. 21

1 Akorinto 14:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Mf 18:26

1 Akorinto 14:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:1, 7
  • +1Ak 14:4, 26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/2007, ptsa. 23-24

1 Akorinto 14:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:10; 14:5

1 Akorinto 14:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:2

1 Akorinto 14:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Akl 3:16
  • +Sl 47:7

1 Akorinto 14:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 1:20

1 Akorinto 14:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:26

1 Akorinto 14:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:6

1 Akorinto 14:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:4

1 Akorinto 14:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 119:99; Aef 4:14; Ahe 5:13
  • +Yer 4:22; Aro 16:19
  • +Afi 3:15; Ahe 5:14; 1Pe 2:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/2007, tsa. 11

    7/15/1993, tsa. 20

    11/15/1987, tsa. 20

1 Akorinto 14:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 28:11
  • +De 28:49; Yer 5:15
  • +Yes 28:12

1 Akorinto 14:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 2:4
  • +Mac 2:13
  • +Mac 2:37

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

1 Akorinto 14:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:11

1 Akorinto 14:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 5:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/1988, ptsa. 13, 15-16

1 Akorinto 14:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 2:47
  • +Yes 45:14; Zek 8:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/1988, ptsa. 15-16, 20

1 Akorinto 14:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:10
  • +Aro 14:19; 2Ak 12:19

1 Akorinto 14:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:5

1 Akorinto 14:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:4

1 Akorinto 14:29

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:1; Aef 4:11
  • +1At 5:21

1 Akorinto 14:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:10

1 Akorinto 14:31

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:6; 1At 5:20
  • +Ahe 10:25

1 Akorinto 14:33

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:40; Aga 5:25; Akl 2:5
  • +Aro 15:33

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 20

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 120

1 Akorinto 14:34

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ti 2:11, 12
  • +1Ak 11:3; Aef 5:22; Akl 3:18; Tit 2:5; 1Pe 3:1
  • +Ge 3:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    9/1/2012, tsa. 9

    3/1/2006, ptsa. 28-29

    Kukambitsirana, tsa. 29

1 Akorinto 14:35

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 11:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/1989, tsa. 6

1 Akorinto 14:36

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 2:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2011, tsa. 14

1 Akorinto 14:37

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 4:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1993, tsa. 31

1 Akorinto 14:39

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:31; 1At 5:20
  • +1Ak 14:27

1 Akorinto 14:40

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:33; Akl 2:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

    Galamukani!,

    No. 1 2020 tsa. 10

    ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, tsa. 49

    Nsanja ya Olonda,

    8/1/1997, tsa. 9

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

1 Akor. 14:11Ak 12:1
1 Akor. 14:1Aro 12:6; 1At 5:20
1 Akor. 14:21Ak 14:5
1 Akor. 14:21Ak 13:2
1 Akor. 14:32Ak 10:8
1 Akor. 14:51Ak 12:30
1 Akor. 14:5Yow 2:28; Mac 2:17; 21:9
1 Akor. 14:51Ak 12:10
1 Akor. 14:6Aga 1:12; 2:2
1 Akor. 14:61Ak 12:8; 2Ak 11:6
1 Akor. 14:7Yob 21:12
1 Akor. 14:8Nu 10:9; Yob 39:25
1 Akor. 14:91Ak 14:19
1 Akor. 14:91Ak 9:26
1 Akor. 14:112Mf 18:26
1 Akor. 14:121Ak 12:1, 7
1 Akor. 14:121Ak 14:4, 26
1 Akor. 14:131Ak 12:10; 14:5
1 Akor. 14:141Ak 14:2
1 Akor. 14:15Akl 3:16
1 Akor. 14:15Sl 47:7
1 Akor. 14:162Ak 1:20
1 Akor. 14:171Ak 14:26
1 Akor. 14:181Ak 14:6
1 Akor. 14:191Ak 14:4
1 Akor. 14:20Sl 119:99; Aef 4:14; Ahe 5:13
1 Akor. 14:20Yer 4:22; Aro 16:19
1 Akor. 14:20Afi 3:15; Ahe 5:14; 1Pe 2:2
1 Akor. 14:21Yes 28:11
1 Akor. 14:21De 28:49; Yer 5:15
1 Akor. 14:21Yes 28:12
1 Akor. 14:22Mac 2:4
1 Akor. 14:22Mac 2:13
1 Akor. 14:22Mac 2:37
1 Akor. 14:231Ak 14:11
1 Akor. 14:24Aef 5:13
1 Akor. 14:25Da 2:47
1 Akor. 14:25Yes 45:14; Zek 8:23
1 Akor. 14:261Ak 12:10
1 Akor. 14:26Aro 14:19; 2Ak 12:19
1 Akor. 14:271Ak 14:5
1 Akor. 14:281Ak 14:4
1 Akor. 14:29Mac 13:1; Aef 4:11
1 Akor. 14:291At 5:21
1 Akor. 14:301Ak 12:10
1 Akor. 14:31Aro 12:6; 1At 5:20
1 Akor. 14:31Ahe 10:25
1 Akor. 14:331Ak 14:40; Aga 5:25; Akl 2:5
1 Akor. 14:33Aro 15:33
1 Akor. 14:341Ti 2:11, 12
1 Akor. 14:341Ak 11:3; Aef 5:22; Akl 3:18; Tit 2:5; 1Pe 3:1
1 Akor. 14:34Ge 3:16
1 Akor. 14:351Ak 11:6
1 Akor. 14:36Yes 2:3
1 Akor. 14:371Yo 4:6
1 Akor. 14:391Ak 12:31; 1At 5:20
1 Akor. 14:391Ak 14:27
1 Akor. 14:401Ak 14:33; Akl 2:5
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
  • 32
  • 33
  • 34
  • 35
  • 36
  • 37
  • 38
  • 39
  • 40
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
1 Akorinto 14:1-40

1 Akorinto

14 Yesetsani kukhala ndi chikondi, komanso pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zauzimu,+ makamaka kunenera.+ 2 Chifukwa wolankhula lilime lachilendo salankhula ndi anthu, koma ndi Mulungu, pakuti palibe amene amamva zonena zake,+ koma amalankhula zinsinsi zopatulika+ mwa mzimu. 3 Komabe, wonenera amathandiza+ anthu ndipo amawalimbikitsa ndi kuwatonthoza ndi mawu ake. 4 Wolankhula lilime lachilendo amadzilimbikitsa yekha, koma wonenera amalimbikitsa mpingo. 5 Tsopano ndikanakonda kuti nonsenu muzilankhula malilime,+ koma ndikuona kuti ndi bwino kuti muzinenera.+ Ndithudi, wonenera amaposa wolankhula malilime achilendo,+ kupatulapo ngati wa malilimeyo amasulira, kuti amange mpingo. 6 Koma pa nthawi ino abale, ngati ineyo ndingabwere kwa inu ndikulankhula malilime, kodi mungapindulepo chiyani ngati sindingakulankhuleni ndi mawu amene ndalandira kuchokera kwa Mulungu,+ kapena ndi mphatso yodziwa zinthu,+ kapena ndi ulosi, kapena ndi chiphunzitso?

7 Chabwino, zinthu zopanda moyo zimamveka kulira kwake,+ kaya chikhale chitoliro kapena zeze. Koma ngati maliridwe ake angokhala amodzi osasinthasintha, kodi n’zotheka kudziwa nyimbo imene ikuimbidwa ndi chitoliro kapena zezeyo? 8 Ndithudi, ngati lipenga likulira mwa mamvekedwe osadziwika bwino, ndani angakonzekere nkhondo?+ 9 Momwemonso, ngati simukulankhula zomveka ndi lilime lanu,+ zingatheke bwanji kudziwa zimene mukunena? Kwenikweni mudzakhala mukulankhula kwa mphepo.+ 10 Pangakhale zinenero zosiyanasiyana padziko lapansi, koma palibe zinenero zimene zilibe tanthauzo. 11 Chotero ngati sindikudziwa tanthauzo la chinenero, ndimakhala mlendo+ kwa wolankhulayo, ndipo wolankhulayo amakhala mlendo kwa ine. 12 Inunso chimodzimodzi, popeza mukufunitsitsa mphatso za mzimu.+ Chotero, yesetsani kukhala nazo zochuluka kuti mumange mpingo.+

13 Choncho amene amalankhula lilime lachilendo apemphere kuti athe kumasulira.+ 14 Pakuti ngati ndikupemphera m’lilime lachilendo, mphatso yanga ya mzimu ndi imene ikupemphera,+ koma maganizo anga amakhala opanda phindu. 15 Ndiye chofunika n’chiyani? Ndipemphere ndi mphatso ya mzimu, koma ndipempherenso ndi maganizo anga. Ndiimbe chitamando ndi mphatso ya mzimu,+ koma ndiimbenso ndi maganizo anga.+ 16 Chifukwa ngati mupereka chitamando ndi mphatso ya mzimu, kodi munthu wamba anganene bwanji “Ame”+ pa kuyamika kwanu, posadziwa zimene mukunena? 17 Zoonadi, mukupereka chiyamiko m’njira yabwino, koma munthu winayo sakulimbikitsidwa.+ 18 Ndimayamika Mulungu kuti ndimalankhula malilime ambiri kuposa nonsenu.+ 19 Ngakhale zili choncho, ndi bwino kuti mumpingo ndilankhule mawu asanu omveka, kutinso ndilangize ena ndi mawuwo, kusiyana n’kulankhula mawu 10,000 m’lilime lachilendo.+

20 Abale, musakhale ana aang’ono pa luntha la kuzindikira,+ koma khalani tiana pa zoipa,+ ndipo pa luntha la kuzindikira khalani aakulu msinkhu.+ 21 M’Chilamulo muli mawu akuti: “‘Anthu awa+ ndidzawalankhula m’malilime a alendo,+ ndipo ndidzawalankhula ndi milomo ya anthu achilendo, koma iwo sadzandimverabe,’ watero Yehova.”+ 22 Chotero malilimewo ndi chizindikiro+ kwa osakhulupirira,+ osati kwa okhulupirira, koma kunenera ndi kwa okhulupirira,+ osati osakhulupirira. 23 Ndiye chifukwa chake, ngati mpingo wonse wasonkhana malo amodzi ndipo onse akulankhula malilime,+ ndiyeno mwalowa anthu osadziwa kalikonse kapena osakhulupirira, kodi sadzanena kuti ndinu amisala? 24 Koma ngati nonse mukunenera, ndiyeno mwalowa winawake wosakhulupirira kapena munthu wamba, iye amadzudzulidwa ndi nonsenu.+ Nonsenu mumamufufuza mosamala. 25 Zobisika za mumtima mwake zimaululika,+ moti adzagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi, n’kulambira Mulungu, ndi kunena kuti: “Zoonadi Mulungu ali pakati panu.”+

26 Ndiyeno zizikhala bwanji, abale? Mukasonkhana pamodzi, wina amakhala ndi salimo, wina chiphunzitso, wina mawu amene walandira kuchokera kwa Mulungu, wina lilime lachilendo, wina kumasulira.+ Zochitika zonse zikhale zolimbikitsa.+ 27 Ndipo ngati pali anthu olankhula lilime lachilendo, asapose awiri kapena atatu, azisiyirana mpata, ndipo wina amasulire.+ 28 Koma ngati palibe womasulira, wa malilimeyo akhale chete mumpingo. Adzilankhule yekha mumtima+ ndipo alankhule kwa Mulungu. 29 Aneneri awiri kapena atatu+ alankhule, ndipo ena onse azindikire tanthauzo la zimene iwo alankhula.+ 30 Koma ngati mneneri wina amene wakhala pansi walandira mawu kuchokera kwa Mulungu,+ woyambayo akhale chete. 31 Pakuti nonse munganenere,+ koma mmodzi ndi mmodzi, kuti onse aphunzire ndi kulimbikitsidwa.+ 32 Ndipo mphatso za mzimu za aneneri ziyenera kulamulidwa ndi aneneri. 33 Pakuti Mulungu si Mulungu wachisokonezo,+ koma wamtendere.+

Mofanana ndi m’mipingo yonse ya oyerawo, 34 akazi akhale chete+ m’mipingo, pakuti sikololeka kuti iwo azilankhula, koma akhale ogonjera,+ monga Chilamulo+ chimanenera. 35 Koma ngati akufuna kumvetsa chinachake, akafunse amuna awo kunyumba, popeza n’zochititsa manyazi+ kuti mkazi azilankhula mumpingo.

36 Kodi mawu a Mulungu anachokera kwa inu,+ kapena anafika kwa inu nokha?

37 Ngati munthu akuganiza kuti ndi mneneri kapena ali ndi mphatso ya mzimu, avomereze zimene ndakulemberanizi, chifukwa ndizo lamulo la Ambuye.+ 38 Koma ngati wina savomereza, akhale. 39 Choncho abale anga, pitirizani kufunafuna mwakhama uneneri,+ komanso musaletse kulankhula malilime.+ 40 Koma zinthu zonse zizichitika moyenera ndi mwadongosolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena