Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nyimbo ya Solomo 7
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Nyimbo ya Solomo 7:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 52:7; Aro 10:15
  • +Sl 110:3
  • +Sl 45:13

Nyimbo ya Solomo 7:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 9:2; Nym 8:2
  • +Nym 2:2

Nyimbo ya Solomo 7:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 4:5

Nyimbo ya Solomo 7:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 1:10; 4:4
  • +Nym 4:1
  • +Nu 21:25; Yos 21:39

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2006, tsa. 20

    11/15/1987, tsa. 25

Nyimbo ya Solomo 7:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 35:2
  • +Nym 6:5
  • +Est 8:15; Nym 3:10
  • +Nym 1:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/1996, tsa. 7

Nyimbo ya Solomo 7:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 4:7

Nyimbo ya Solomo 7:7

Mawu a M'munsi

  • *

    Umenewu ndi mtundu wa kanjedza amene amamera ku Palesitina.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 92:12
  • +Nym 7:3; 8:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2007, tsa. 32

Nyimbo ya Solomo 7:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 5:28; 1Ti 5:2

Nyimbo ya Solomo 7:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 104:15
  • +Miy 23:31

Nyimbo ya Solomo 7:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 2:16; 6:3
  • +Nym 2:14

Nyimbo ya Solomo 7:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 8:1
  • +Nym 1:14; 4:13

Nyimbo ya Solomo 7:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 6:11
  • +Nym 2:13
  • +De 8:8; Nym 6:11
  • +Nym 1:4; 4:10

Nyimbo ya Solomo 7:13

Mawu a M'munsi

  • *

    “Mandereki” ndi chitsamba cha m’gulu la mbatata, chimene chimabereka zipatso.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 30:14
  • +Nym 4:16

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Nyimbo 7:1Yes 52:7; Aro 10:15
Nyimbo 7:1Sl 110:3
Nyimbo 7:1Sl 45:13
Nyimbo 7:2Miy 9:2; Nym 8:2
Nyimbo 7:2Nym 2:2
Nyimbo 7:3Nym 4:5
Nyimbo 7:4Nym 1:10; 4:4
Nyimbo 7:4Nym 4:1
Nyimbo 7:4Nu 21:25; Yos 21:39
Nyimbo 7:5Yes 35:2
Nyimbo 7:5Nym 6:5
Nyimbo 7:5Est 8:15; Nym 3:10
Nyimbo 7:5Nym 1:4
Nyimbo 7:6Nym 4:7
Nyimbo 7:7Sl 92:12
Nyimbo 7:7Nym 7:3; 8:10
Nyimbo 7:8Mt 5:28; 1Ti 5:2
Nyimbo 7:9Sl 104:15
Nyimbo 7:9Miy 23:31
Nyimbo 7:10Nym 2:16; 6:3
Nyimbo 7:10Nym 2:14
Nyimbo 7:11Nym 8:1
Nyimbo 7:11Nym 1:14; 4:13
Nyimbo 7:12Nym 6:11
Nyimbo 7:12Nym 2:13
Nyimbo 7:12De 8:8; Nym 6:11
Nyimbo 7:12Nym 1:4; 4:10
Nyimbo 7:13Ge 30:14
Nyimbo 7:13Nym 4:16
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Nyimbo ya Solomo 7:1-13

Nyimbo ya Solomo

7 “Mapazi ako akukongola kwambiri munsapato zako,+ iwe mwana wamkazi+ wodzipereka. Ntchafu zako n’zoumbidwa bwino ngati zinthu zokongoletsera,+ ngati ntchito ya manja a munthu waluso. 2 Mchombo wako uli ngati mbale yozungulira. Vinyo wosakaniza+ asasowepo. Mimba yako ili ngati mulu wa tirigu, wotchingidwa ndi maluwa.+ 3 Mabere ako awiri ali ngati ana awiri aang’ono, ngati ana amapasa a insa yaikazi.+ 4 Khosi lako+ lili ngati nsanja ya mnyanga wa njovu. Maso ako+ ali ngati maiwe a ku Hesiboni,+ amene ali pafupi ndi chipata cha Bati-rabimu. Mphuno yako ili ngati nsanja ya Lebanoni, imene inayang’ana cha ku Damasiko. 5 Mutu wako ndi wokwezeka ngati Karimeli.+ Tsitsi+ la m’mutu mwako lili ngati ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira,+ ndipo mfumu yatengeka nalo tsitsi lako lalitalilo.+ 6 Iwe mtsikana wokondedwa, ndiwe wokongola, ndipo ndiwe wosangalatsa kuposa zinthu zina zonse zosangalatsa mtima.+ 7 Msinkhu wako uli ngati mtengo wa kanjedza,*+ ndipo mabere ako+ ali ngati zipatso zake. 8 Ine ndinati, ‘Ndikwera mtengo wa kanjedza kuti ndikathyole nthambi zake zokhala ndi zipatso.’+ Mabere ako akhale ngati zipatso za mpesa, ndipo mpweya wa m’kamwa mwako ununkhire ngati maapozi. 9 M’kamwa mwako mukhale ngati vinyo wabwino kwambiri+ amene amatsetserekera kukhosi kwa wokondedwa wanga mwamyaa,+ amene amayenderera pang’onopang’ono pamilomo ya anthu amene akugona.”

10 “Wachikondi wangayo, ine ndine wake,+ ndipo iye akulakalaka ineyo.+ 11 Bwera wachikondi wanga. Tiye tipite kumunda.+ Tiye tikakhale pakati pa mitengo ya maluwa ofiirira.+ 12 Tiye tilawirire m’mawa tipite kuminda ya mpesa. Tikaone ngati mitengo ya mpesa yaphukira,+ ngati yatuluka maluwa,+ ndiponso ngati mitengo ya makangaza yachita maluwa.+ Kumeneko ndikakusonyeza chikondi changa.+ 13 Zipatso za mandereki*+ zikununkhira, ndipo pafupi ndi makomo olowera kunyumba zathu pali zipatso zosiyanasiyana zokoma kwambiri.+ Ndakusungira zipatso zatsopano ndi zakale zomwe, iwe wachikondi wanga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena