Masalimo
Nyimbo ya Davide.
4 Ngakhale ndikuyenda m’chigwa cha mdima wandiweyani,+
Sindikuopa kanthu,+
Pakuti inu muli ndi ine.+
Chibonga chanu ndi ndodo yanu ndi zimene zimandilimbikitsa.+
Palibe Vidiyo.
Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.
Nyimbo ya Davide.
4 Ngakhale ndikuyenda m’chigwa cha mdima wandiweyani,+
Sindikuopa kanthu,+
Pakuti inu muli ndi ine.+
Chibonga chanu ndi ndodo yanu ndi zimene zimandilimbikitsa.+