Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 17
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 17:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:1
  • +1Ak 6:15; Yak 4:4
  • +Yes 57:20; Yer 51:13; Chv 17:15; 19:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2019, ptsa. 10-11

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, tsa. 220

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 235-244

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1989, ptsa. 5-7

    4/15/1989, ptsa. 7-8

    4/1/1989, tsa. 3

Chivumbulutso 17:2

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 7.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 47:5; Yak 4:4; Chv 18:9
  • +Yer 51:7; Chv 14:8; 18:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, tsa. 220

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 235-244

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, ptsa. 7-8, 10-12

    4/1/1989, ptsa. 3, 5-6

Chivumbulutso 17:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 37:1; Chv 1:10
  • +Chv 13:15
  • +Mko 3:29
  • +Chv 17:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2012, tsa. 17

    9/1/1989, tsa. 7

    4/15/1989, ptsa. 12-13

    9/1/1987, tsa. 20

    2/1/1986, tsa. 7

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 240-243

    Galamukani!,

    9/8/1987, tsa. 9

Chivumbulutso 17:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 5:29; Lu 16:19
  • +Mt 27:28
  • +Chv 18:12, 19
  • +Yer 51:7
  • +De 29:17; Yes 66:3
  • +Aro 1:24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 243-245

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, ptsa. 12-13

    4/1/1989, ptsa. 5-6

Chivumbulutso 17:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2At 2:7
  • +Chv 19:2
  • +Eze 22:2; Chv 18:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2008, tsa. 9

    2/1/1990, tsa. 17

    4/15/1989, ptsa. 12-13

    4/1/1989, tsa. 3

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 243-244

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 209-210

Chivumbulutso 17:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 18:24; 19:2
  • +Chv 6:9
  • +Eze 28:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 243-246

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1989, tsa. 6

    4/15/1989, tsa. 13

    4/1/1989, ptsa. 8-9

Chivumbulutso 17:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:5
  • +Chv 17:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 246-247

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, ptsa. 13-14

Chivumbulutso 17:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:15
  • +Chv 20:1
  • +Eks 32:32; Sl 69:28; Afi 4:3
  • +Chv 13:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 247-251

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1988, ptsa. 27-28

    9/1/1987, ptsa. 20, 29

    2/1/1986, tsa. 7

    Galamukani!,

    11/8/1987, tsa. 28

Chivumbulutso 17:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 24:15; Yak 3:17
  • +Chv 17:7
  • +Yer 51:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 251-253

Chivumbulutso 17:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 46:2; 51:11; Da 8:20, 21; Zef 2:13
  • +Yoh 19:15
  • +Da 8:23
  • +Chv 13:11; 19:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 9-10

    Galamukani!,

    5/2011, ptsa. 15-16

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 251-253

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1988, tsa. 28

    5/15/1988, ptsa. 24-26

    5/1/1988, tsa. 28

    2/1/1988, tsa. 22

    2/1/1986, ptsa. 5-6

Chivumbulutso 17:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2022, tsa. 5

    5/2022, tsa. 10

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 253-254

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1988, tsa. 28

    2/1/1986, tsa. 7

Chivumbulutso 17:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 254-255

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1988, ptsa. 19-20

Chivumbulutso 17:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 2:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 254-255

Chivumbulutso 17:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 1:29; Chv 5:6
  • +Mt 28:18; Mac 2:36; 1Ti 6:15
  • +Chv 19:15
  • +Aro 16:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    “Wotsatira Wanga,” tsa. 23

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, tsa. 19

    6/15/2012, tsa. 18

    1/1/2007, tsa. 27

    2/15/1998, ptsa. 16-17

    10/15/1988, ptsa. 19-20

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 254-256, 276

Chivumbulutso 17:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 57:20; Yer 51:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 256

    Galamukani!,

    11/8/1996, ptsa. 5-6

Chivumbulutso 17:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:24; Chv 17:12
  • +Chv 17:8
  • +Chv 17:7
  • +Ge 38:24; Le 21:9; Chv 18:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 11-14

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2019, ptsa. 10-11

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, tsa. 15

    6/15/2012, tsa. 18

    2/1/2004, tsa. 21

    6/1/1996, tsa. 18

    3/1/1994, tsa. 20

    10/15/1988, ptsa. 16-17

    11/1/1987, tsa. 28

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 223

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 256-258

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 36-37

Chivumbulutso 17:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yos 11:20; Miy 21:1; Yer 51:12
  • +Chv 17:12
  • +Yes 55:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 11-14

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2019, ptsa. 14-15

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2012, tsa. 5

    6/15/2012, tsa. 18

    2/1/2004, tsa. 21

    3/1/1994, tsa. 20

    5/15/1989, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 257-258

    Ulosi wa Danieli, tsa. 282

Chivumbulutso 17:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:5
  • +Yes 47:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, tsa. 220

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 258

    Galamukani!,

    11/8/1996, ptsa. 5-6

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1989, tsa. 4

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 17:1Chv 16:1
Chiv. 17:11Ak 6:15; Yak 4:4
Chiv. 17:1Yes 57:20; Yer 51:13; Chv 17:15; 19:2
Chiv. 17:2Yes 47:5; Yak 4:4; Chv 18:9
Chiv. 17:2Yer 51:7; Chv 14:8; 18:3
Chiv. 17:3Eze 37:1; Chv 1:10
Chiv. 17:3Chv 13:15
Chiv. 17:3Mko 3:29
Chiv. 17:3Chv 17:9
Chiv. 17:4Da 5:29; Lu 16:19
Chiv. 17:4Mt 27:28
Chiv. 17:4Chv 18:12, 19
Chiv. 17:4Yer 51:7
Chiv. 17:4De 29:17; Yes 66:3
Chiv. 17:4Aro 1:24
Chiv. 17:52At 2:7
Chiv. 17:5Chv 19:2
Chiv. 17:5Eze 22:2; Chv 18:5
Chiv. 17:6Chv 18:24; 19:2
Chiv. 17:6Chv 6:9
Chiv. 17:6Eze 28:19
Chiv. 17:7Chv 17:5
Chiv. 17:7Chv 17:3
Chiv. 17:8Chv 13:15
Chiv. 17:8Chv 20:1
Chiv. 17:8Eks 32:32; Sl 69:28; Afi 4:3
Chiv. 17:8Chv 13:8
Chiv. 17:9Mt 24:15; Yak 3:17
Chiv. 17:9Chv 17:7
Chiv. 17:9Yer 51:25
Chiv. 17:10Yer 46:2; 51:11; Da 8:20, 21; Zef 2:13
Chiv. 17:10Yoh 19:15
Chiv. 17:10Da 8:23
Chiv. 17:10Chv 13:11; 19:20
Chiv. 17:11Chv 17:8
Chiv. 17:12Da 7:24
Chiv. 17:13Sl 2:2
Chiv. 17:14Yoh 1:29; Chv 5:6
Chiv. 17:14Mt 28:18; Mac 2:36; 1Ti 6:15
Chiv. 17:14Chv 19:15
Chiv. 17:14Aro 16:20
Chiv. 17:15Yes 57:20; Yer 51:13
Chiv. 17:16Da 7:24; Chv 17:12
Chiv. 17:16Chv 17:8
Chiv. 17:16Chv 17:7
Chiv. 17:16Ge 38:24; Le 21:9; Chv 18:8
Chiv. 17:17Yos 11:20; Miy 21:1; Yer 51:12
Chiv. 17:17Chv 17:12
Chiv. 17:17Yes 55:11
Chiv. 17:18Chv 17:5
Chiv. 17:18Yes 47:5
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 17:1-18

Chivumbulutso

17 Mmodzi wa angelo 7 amene anali ndi mbale 7+ aja, anabwera n’kundiuza kuti: “Bwera, ndikuonetsa chiweruzo cha hule lalikulu+ lokhala pamadzi ambiri,+ 2 limene mafumu a dziko lapansi anachita nalo dama,+ ndipo linaledzeretsa anthu okhala padziko lapansi ndi vinyo wa dama* lake.”+

3 Mu mphamvu ya mzimu,+ mngeloyo ananditengera kuchipululu. Ndipo ndinaona mkazi atakhala pachilombo+ chofiira kwambiri, chodzaza ndi mayina onyoza Mulungu.+ Chinali ndi mitu 7,+ ndi nyanga 10. 4 Mkaziyo anavala zovala zofiirira+ ndi zofiira kwambiri.+ Anadzikongoletsa ndi golide, ndi mwala winawake wamtengo wapatali, ndiponso ngale.+ M’dzanja lake, anali ndi kapu yagolide+ yodzaza ndi zonyansa+ ndi zinthu zodetsedwa zokhudzana ndi dama lake.+ 5 Pamphumi pake panalembedwa dzina lachinsinsi+ lakuti: “Babulo Wamkulu, mayi wa mahule+ ndi wa zonyansa za padziko lapansi.”+ 6 Ndipo ndinaona kuti mkaziyo anali ataledzera ndi magazi+ a oyera, ndiponso magazi a mboni za Yesu.+

Nditamuona mkaziyo, ndinadabwa kwambiri.+ 7 Koma mngelo uja anandifunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukudabwa? Ndikuuza chinsinsi cha mkazi ameneyu,+ ndi cha chilombo chimene wakwerapo, chokhala ndi mitu 7 ndi nyanga 10:+ 8 Chilombo chimene waona, chinalipo,+ tsopano palibe, komabe chili pafupi kutuluka kuphompho,+ ndipo chidzapita ku chiwonongeko. Anthu okhala padziko lapansi akaona kuti chilombocho chinalipo, tsopano palibe, komabe chidzakhalapo, adzadabwa kwambiri pochita nacho chidwi. Koma mayina awo sanalembedwe mumpukutu wa moyo+ kuyambira pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+

9 “Apa m’pamene pakufunika kuchenjera ndiponso kukhala ndi nzeru:+ Mitu 7+ ikuimira mapiri 7,+ amene mkazi uja amakhala pamwamba pake. 10 Palinso mafumu 7. Asanu agwa,+ imodzi ilipo,+ inayo sinafikebe.+ Koma ikafika, ikufunika kudzakhala kanthawi kochepa.+ 11 Ndipo chilombo chimene chinalipo, koma tsopano palibe,+ n’chimenenso chili mfumu ya 8, koma yotuluka mwa mafumu 7 aja, ndipo ikupita ku chiwonongeko.

12 “Nyanga 10 zimene unaona zija, zikuimira mafumu 10+ amene sanalandirebe ufumu wawo. Koma adzalandira ulamuliro monga mafumu ndipo adzalamulira limodzi ndi chilombo kwa ola limodzi. 13 Mafumuwa maganizo awo ndi amodzi, choncho adzapereka mphamvu zawo ndi ulamuliro wawo kwa chilombocho.+ 14 Iwowa adzamenyana ndi Mwanawankhosa,+ koma pakuti iye ndiye Mbuye wa ambuye ndi Mfumu ya mafumu,+ Mwanawankhosayo adzawagonjetsa.+ Komanso oitanidwa aja, amene ali osankhidwa mwapadera ndi okhulupirika, nawonso adzagonjetsa naye limodzi.”+

15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+ 16 Nyanga 10+ waziona zija, komanso chilombo,+ zimenezi zidzadana nalo hulelo.+ Zidzalisakaza ndi kulisiya lamaliseche. Zidzadya minofu yake ndi kulinyeketsa ndi moto.+ 17 Pakuti Mulungu anaika izi m’mitima yawo kuti zichite monga mwa maganizo ake,+ kuti zikwaniritse maganizo awo amodzi, mwa kupereka ufumu wawo kwa chilombo,+ kufikira mawu a Mulungu atakwaniritsidwa.+ 18 Ndipo mkazi+ amene unamuonayo akuimira mzinda waukulu umene ukulamulira mafumu a dziko lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena