Genesis 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Mulungu anapanga mlengalenga nʼkulekanitsa madzi kuti ena akhale pansi pa mlengalenga ndipo ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi. Genesis 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nowa anali ndi zaka 600 pamene chigumula chinachitika padziko lapansi.+ Genesis 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mʼchaka cha 600 cha moyo wa Nowa, mʼmwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli madzi onse akumwamba anaphulika ndipo zitseko zotchingira madzi akumwamba zinatseguka.+
7 Choncho Mulungu anapanga mlengalenga nʼkulekanitsa madzi kuti ena akhale pansi pa mlengalenga ndipo ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi.
11 Mʼchaka cha 600 cha moyo wa Nowa, mʼmwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli madzi onse akumwamba anaphulika ndipo zitseko zotchingira madzi akumwamba zinatseguka.+