Genesis 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Mulungu anapanga mlengalenga nʼkulekanitsa madzi kuti ena akhale pansi pa mlengalenga ndipo ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi. Genesis 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Madzi onse akumwamba anasiya kutuluka komanso zitseko zotchingira madziwo zinatsekeka, choncho chimvula chinasiya kugwa kuchokera kumwamba.+
7 Choncho Mulungu anapanga mlengalenga nʼkulekanitsa madzi kuti ena akhale pansi pa mlengalenga ndipo ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi.
2 Madzi onse akumwamba anasiya kutuluka komanso zitseko zotchingira madziwo zinatsekeka, choncho chimvula chinasiya kugwa kuchokera kumwamba.+