Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:19, 20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mʼchingalawacho udzalowetsemo chamoyo cha mtundu uliwonse.+ Udzazilowetse ziwiriziwiri, chachimuna ndi chachikazi,+ kuti zidzasungike zamoyo limodzi ndi iwe. 20 Udzalowe nazo ziwiriziwiri za mtundu uliwonse. Zolengedwa zouluka monga mwa mitundu yawo, nyama zoweta monga mwa mitundu yawo, nyama zonse zokwawa panthaka monga mwa mitundu yawo, kuti zidzasungike zamoyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena