-
Genesis 35:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno Yakobo anauza anthu a mʼbanja lake ndi onse amene anali naye kuti: “Chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu.+ Dziyeretseni ndipo sinthani zovala zanu. 3 Mukatero, tinyamuke tipite ku Beteli. Kumeneko ndikamangira guwa lansembe Mulungu woona, amene anandiyankha pa tsiku la kusautsika kwanga, ndipo wakhala nane kulikonse kumene ndapita.”+
-