Genesis 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Komanso, Mulungu anawadalitsa nʼkuwauza kuti: “Muberekane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi+ ndipo muziliyangʼanira.+ Muyangʼanirenso+ nsomba zamʼnyanja ndi zamoyo zouluka mumlengalenga, komanso chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.” Genesis 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero Yehova Mulungu anadzala munda ku Edeni,+ chakumʼmawa, ndipo mʼmundamo anaikamo munthu amene anamuumba uja.+ Salimo 115:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kunena za kumwamba, kumwamba ndi kwa Yehova,+Koma dziko lapansi analipereka kwa ana a anthu.+
28 Komanso, Mulungu anawadalitsa nʼkuwauza kuti: “Muberekane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi+ ndipo muziliyangʼanira.+ Muyangʼanirenso+ nsomba zamʼnyanja ndi zamoyo zouluka mumlengalenga, komanso chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.”
8 Zitatero Yehova Mulungu anadzala munda ku Edeni,+ chakumʼmawa, ndipo mʼmundamo anaikamo munthu amene anamuumba uja.+