Genesis 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Patapita nthawi, Yakobo anamva zimene ana aamuna a Labani ankanena kuti: “Yakobo watenga zinthu zonse za bambo athu, ndipo chuma chonse chimene ali nachochi chachokera kwa bambo athu.”+
31 Patapita nthawi, Yakobo anamva zimene ana aamuna a Labani ankanena kuti: “Yakobo watenga zinthu zonse za bambo athu, ndipo chuma chonse chimene ali nachochi chachokera kwa bambo athu.”+