Genesis 31:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Mulungu wa Abulahamu+ ndi Mulungu wa Nahori, yemwe ndi Mulungu wa bambo awo, atiweruze.” Ndipo Yakobo analumbira mʼdzina la Mulungu amene bambo ake Isaki ankamuopa.+
53 Mulungu wa Abulahamu+ ndi Mulungu wa Nahori, yemwe ndi Mulungu wa bambo awo, atiweruze.” Ndipo Yakobo analumbira mʼdzina la Mulungu amene bambo ake Isaki ankamuopa.+