Genesis 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yehova anauza Yakobo kuti: “Bwerera kudziko la makolo ako ndi kwa abale ako,+ ndipo ine ndidzapitiriza kukuthandiza.” Genesis 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndine Mulungu woona wa ku Beteli+ kumene unadzoza mwala wachikumbutso kuja, kumenenso unachita lonjezo kwa ine.+ Tsopano nyamuka, uchoke kudziko lino, ubwerere kudziko limene unabadwira.’”+
3 Kenako Yehova anauza Yakobo kuti: “Bwerera kudziko la makolo ako ndi kwa abale ako,+ ndipo ine ndidzapitiriza kukuthandiza.”
13 Ndine Mulungu woona wa ku Beteli+ kumene unadzoza mwala wachikumbutso kuja, kumenenso unachita lonjezo kwa ine.+ Tsopano nyamuka, uchoke kudziko lino, ubwerere kudziko limene unabadwira.’”+