Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Inu Mʼbusa wa Isiraeli, mvetserani,Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+ Inu amene mwakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi,+Onetsani kuwala kwanu.* Yesaya 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ Mulungu wa Isiraeli, wokhala pamwamba* pa akerubi, inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse apadziko lapansi. Inuyo munapanga kumwamba ndi dziko lapansi. Ezekieli 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno ulemerero wa Yehova+ unachoka pa akerubi nʼkupita pakhomo la nyumba yopatulika ndipo mtambo unayamba kudzaza nyumbayo pangʼonopangʼono.+ Komanso ulemerero wowala wa Yehova unadzaza mʼbwalo lonse la nyumbayo.
80 Inu Mʼbusa wa Isiraeli, mvetserani,Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+ Inu amene mwakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi,+Onetsani kuwala kwanu.*
16 “Inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ Mulungu wa Isiraeli, wokhala pamwamba* pa akerubi, inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse apadziko lapansi. Inuyo munapanga kumwamba ndi dziko lapansi.
4 Ndiyeno ulemerero wa Yehova+ unachoka pa akerubi nʼkupita pakhomo la nyumba yopatulika ndipo mtambo unayamba kudzaza nyumbayo pangʼonopangʼono.+ Komanso ulemerero wowala wa Yehova unadzaza mʼbwalo lonse la nyumbayo.