Genesis 34:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Hamori anawauza kuti: “Mwana wanga Sekemu wamukonda mtsikana wanuyu ndi mtima wonse. Chonde, mupatseni kuti akhale mkazi wake. 9 Tiyeni tichite mgwirizano kuti tizikwatirana. Muzitipatsa ana anu aakazi, inunso muzitenga ana athu aakazi.+
8 Ndiyeno Hamori anawauza kuti: “Mwana wanga Sekemu wamukonda mtsikana wanuyu ndi mtima wonse. Chonde, mupatseni kuti akhale mkazi wake. 9 Tiyeni tichite mgwirizano kuti tizikwatirana. Muzitipatsa ana anu aakazi, inunso muzitenga ana athu aakazi.+