Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 28:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamwamba pa masitepewo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti:

      “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbadwa* zako.+

  • Genesis 32:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Atatero, Yakobo anati: “Mulungu wa kholo langa Abulahamu, Mulungu wa bambo anga Isaki, inu Yehova munandiuza kuti, ‘Bwerera kudziko lakwanu kwa abale ako, ndipo ndidzakusamalira.’+

  • Mateyu 22:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakoboʼ?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+

  • Machitidwe 7:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 ‘Ine ndine Mulungu wa makolo ako, Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo.’+ Mose anayamba kunjenjemera ndipo sanafunenso kupita pafupi ndi chitsambacho kuti akaonetsetse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena